Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo sinawamvere, anaiyankha kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese. Pitani kwa milungu yanu+ Aisiraeli. Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, anayamba kubwerera kumahema awo.

  • 1 Mafumu 14:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ndipo ndinang’amba+ ufumuwo kuuchotsa kunyumba ya Davide ndi kuupereka kwa iwe, koma iwe sunakhale ngati Davide mtumiki wanga. Iyeyo anasunga malamulo anga ndi kunditsatira ndi mtima wake wonse mwa kuchita zinthu zoyenera zokhazokha m’maso mwanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena