Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndichita zimenezi chifukwa iwo andisiya ine+ n’kuyamba kugwadira Asitoreti+ mulungu wamkazi wa Asidoni, Kemosi+ mulungu wa Amowabu, ndi Milikomu+ mulungu wa ana a Amoni. Sanayende m’njira zanga mwa kuchita choyenera pamaso panga ndi kutsatira malamulo anga ndi zigamulo zanga monga anachitira Davide bambo a Solomo.

  • 1 Mafumu 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+

  • Machitidwe 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena