Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tidzafuula mokondwera chifukwa cha chipulumutso chanu,+

      Tidzakweza mbendera zathu m’dzina la Mulungu wathu.+

      Yehova akwaniritse zopempha zanu zonse.+

  • Salimo 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+

      Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+

  • Salimo 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+

      Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+

  • Salimo 95:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+

      Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+

  • Mika 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+

  • Zefaniya 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Fuula mosangalala iwe mwana wamkazi wa Ziyoni! Fuula mokondwera+ iwe Isiraeli! Sangalala ndi kukondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena