Zefaniya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Fuula mosangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni!* Fuula chifukwa chopambana, iwe Isiraeli!+ Sangalala ndiponso kondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!*+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 24
14 Fuula mosangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni!* Fuula chifukwa chopambana, iwe Isiraeli!+ Sangalala ndiponso kondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!*+