Salimo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tidzafuula mosangalala chifukwa cha mmene mwatipulumutsira,+Tidzakweza mbendera zathu mʼdzina la Mulungu wathu.+ Yehova akwaniritse zopempha zanu zonse.
5 Tidzafuula mosangalala chifukwa cha mmene mwatipulumutsira,+Tidzakweza mbendera zathu mʼdzina la Mulungu wathu.+ Yehova akwaniritse zopempha zanu zonse.