Salimo 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu zanu.+Mʼmawa ndidzanena mosangalala za chikondi chanu chokhulupirika. Chifukwa inu ndinu malo anga othawirako otetezeka,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya mavuto.+
16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu zanu.+Mʼmawa ndidzanena mosangalala za chikondi chanu chokhulupirika. Chifukwa inu ndinu malo anga othawirako otetezeka,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya mavuto.+