Salimo 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+
16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+