Yobu 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wamphamvuyonse sitikumudziwa.+Iye ali ndi mphamvu zambiri,+Ndipo sadzanyoza+ chilungamo+ ndi kulungama kochuluka.+ Salimo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, mukhale wokwezeka mu mphamvu zanu.+Tidzaimba ndi kutamanda mphamvu zanu.+ Salimo 106:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+Kuti mphamvu zake zidziwike.+ Salimo 145:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo adzanena za ulemerero wa ufumu wanu.+Ndi kulankhula za mphamvu zanu,+
23 Wamphamvuyonse sitikumudziwa.+Iye ali ndi mphamvu zambiri,+Ndipo sadzanyoza+ chilungamo+ ndi kulungama kochuluka.+