Salimo 89:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+ Salimo 101:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 101 Ndidzaimba za kukoma mtima kwanu kosatha ndi chiweruzo chanu.+Inu Yehova, ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani.+ Aefeso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatero kuti kukoma mtima kwakukulu kwaulemerero+ kumene anatisonyeza kudzera mwa wokondedwa wake+ kutamandike.+
89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+
101 Ndidzaimba za kukoma mtima kwanu kosatha ndi chiweruzo chanu.+Inu Yehova, ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani.+
6 Anatero kuti kukoma mtima kwakukulu kwaulemerero+ kumene anatisonyeza kudzera mwa wokondedwa wake+ kutamandike.+