Aefeso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anachita zimenezi kuti iye atamandike chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu+ kwaulemerero kumene anatisonyeza kudzera mwa mwana wake wokondedwa.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,6/15/2002, ptsa. 5-6
6 Anachita zimenezi kuti iye atamandike chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu+ kwaulemerero kumene anatisonyeza kudzera mwa mwana wake wokondedwa.+