Salimo 89:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+ Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+
89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+