Salimo 35:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma moyo wanga ukondwere mwa Yehova.+Usangalale chifukwa cha chipulumutso chake.+ Salimo 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+ Salimo 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+ Luka 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mzimu wanga sungaleke kusefukira+ ndi chimwemwe mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga.+
14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+
16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+