1 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+ Habakuku 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndidzakondwerabe mwa Yehova+ ndipo ndidzasangalala mwa Mulungu wachipulumutso changa.+
2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+