Salimo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+ Salimo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+
5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+
21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+