Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+ Aheberi 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tikufuna kuti aliyense wa inu apitirize kuonetsa khama limene anali nalo poyamba, kuti chiyembekezo+ chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+
31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+
11 Koma tikufuna kuti aliyense wa inu apitirize kuonetsa khama limene anali nalo poyamba, kuti chiyembekezo+ chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+