Salimo 119:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzakutamandani ndi mtima wowongoka,+Pamene ndikuphunzira zigamulo zanu zolungama.+ Aefeso 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa chifukwa chimenechi, lekani kukhala opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira+ chifuniro+ cha Yehova.
17 Pa chifukwa chimenechi, lekani kukhala opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira+ chifuniro+ cha Yehova.