1 Samueli 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+ 1 Samueli 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Samueli anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Inuyo mwachita choipa chachikulu chimenechi. Ngakhale kuti zili choncho, musapatuke n’kusiya kutsatira Yehova,+ koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse.+
17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+
20 Pamenepo Samueli anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Inuyo mwachita choipa chachikulu chimenechi. Ngakhale kuti zili choncho, musapatuke n’kusiya kutsatira Yehova,+ koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse.+