Salimo 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+ Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.+Iye ali pafupi ndi onse amene amamuitana m’choonadi,+
6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+