Yesaya 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova ndikukupemphani kuti chonde, mukumbukire+ kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse+ komanso ndachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:3 Yesaya 1, tsa. 394
3 “Yehova ndikukupemphani kuti chonde, mukumbukire+ kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse+ komanso ndachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.