Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake. Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”