Mateyu 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma kuti tisawakhumudwitse,+ pita kunyanja, ukaponye mbedza, ndipo ukatenge nsomba yoyambirira kuwedza. Ukakaikanula kukamwa kwake, ukapezako khobidi limodzi lasiliva.* Ukalitenge n’kukhomera msonkho wako ndi wanga.”+ Mateyu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+ 1 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma muzikhalabe osamala kuti ufulu wanuwo usakhale chopunthwitsa kwa ofooka.+ 1 Akorinto 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pewani kukhala okhumudwitsa+ kwa Ayuda, ngakhalenso kwa Agiriki, ndi kwa mpingo wa Mulungu,
27 Koma kuti tisawakhumudwitse,+ pita kunyanja, ukaponye mbedza, ndipo ukatenge nsomba yoyambirira kuwedza. Ukakaikanula kukamwa kwake, ukapezako khobidi limodzi lasiliva.* Ukalitenge n’kukhomera msonkho wako ndi wanga.”+
6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+