Aroma 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa. 1 Akorinto 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero ngati chakudya chikukhumudwitsa+ m’bale wanga, sindidzadyanso nyama m’pang’ono pomwe, kuti ndisakhumudwitse m’bale wanga.+ 1 Akorinto 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pewani kukhala okhumudwitsa+ kwa Ayuda, ngakhalenso kwa Agiriki, ndi kwa mpingo wa Mulungu, 2 Akorinto 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sitikuchita chilichonse chokhumudwitsa,+ kuti utumiki wathu usapezedwe chifukwa.+
13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa.
13 Chotero ngati chakudya chikukhumudwitsa+ m’bale wanga, sindidzadyanso nyama m’pang’ono pomwe, kuti ndisakhumudwitse m’bale wanga.+