Aroma 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ngati m’bale wako akuvutika maganizo chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukuyendanso m’chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera+ chifukwa cha zakudya zanu.
15 Chifukwa ngati m’bale wako akuvutika maganizo chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukuyendanso m’chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera+ chifukwa cha zakudya zanu.