Mateyu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+ Aroma 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndi bwino kusadya nyama kapena kusamwa vinyo kapena kusachita kalikonse kamene kamakhumudwitsa m’bale wako.+ 2 Akorinto 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndani ali wofooka,+ ine osakhalanso wofooka? Ndani wakhumudwitsidwa, ine osakwiya nazo?
6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timakhulupirira mwa ine, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero+ m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumumiza m’nyanja yaikulu.+
21 Ndi bwino kusadya nyama kapena kusamwa vinyo kapena kusachita kalikonse kamene kamakhumudwitsa m’bale wako.+