Yesaya 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kumeneko kudzakhala msewu waukulu+ ndipo udzatchedwa Msewu wa Chiyero.+ Munthu wodetsedwa sadzayendamo.+ Amene adzayendemo ndi munthu yekhayo amene ali woyenerera. Palibe anthu opusa amene azidzayendayendamo. Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Yesaya 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+
8 Kumeneko kudzakhala msewu waukulu+ ndipo udzatchedwa Msewu wa Chiyero.+ Munthu wodetsedwa sadzayendamo.+ Amene adzayendemo ndi munthu yekhayo amene ali woyenerera. Palibe anthu opusa amene azidzayendayendamo.
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+