Yesaya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+ monga mmene panalili msewu umodzi umene Aisiraeli anayendamo m’tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo. Yesaya 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzachititsa kuti mapiri anga onse akhale njira, ndipo misewu yanga yonse idzakhala pamalo okwera.+ Yesaya 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+ Yeremiya 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Udziikire zizindikiro za mumsewu. Udziikire zikwangwani.+ Ika mtima wako panjirayo, njira imene uyenera kuyendamo.+ Bwerera iwe namwali wa Isiraeli. Bwerera kumizinda yakoyi.+
16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+ monga mmene panalili msewu umodzi umene Aisiraeli anayendamo m’tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo.
11 Ndidzachititsa kuti mapiri anga onse akhale njira, ndipo misewu yanga yonse idzakhala pamalo okwera.+
10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+
21 “Udziikire zizindikiro za mumsewu. Udziikire zikwangwani.+ Ika mtima wako panjirayo, njira imene uyenera kuyendamo.+ Bwerera iwe namwali wa Isiraeli. Bwerera kumizinda yakoyi.+