Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Aliyense amene ali pakati panu mwa anthu onse amene amamutumikira, Mulungu wake akhale naye.+ Choncho apite ku Yerusalemu m’dziko la Yuda n’kukamanganso nyumba ya Yehova Mulungu wa Isiraeli, yomwe inali ku Yerusalemu.+ Iye ndiye Mulungu woona.+

  • Yesaya 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+

  • Yesaya 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Inu nonse okhala panthaka ndi inu okhala m’dziko lapansi,+ mudzaona chinthu chooneka ngati chizindikiro chimene chimaikidwa pamapiri,+ ndipo mudzamva zofanana ndi kulira kwa lipenga.+

  • Yesaya 49:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,+ ndipo anthu a mitundu yosiyanasiyana ndidzawakwezera chizindikiro.+ Iwo adzakubweretsera ana ako aamuna atawanyamulira pachifuwa, ndipo ana ako aakazi adzawanyamulira paphewa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena