20 Kenako Davide anauza Solomo mwana wake kuti: “Limba mtima,+ ugwire ntchitoyi mwamphamvu. Usaope+ kapena kuchita mantha+ chifukwa Yehova Mulungu, Mulungu wanga, ali ndi iwe.+ Sadzakutaya+ kapena kukusiya, kufikira ntchito yonse yokhudza utumiki wa nyumba ya Yehova itatha.