Yesaya 57:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno wina adzati, ‘Anthu inu, konzani msewu! Konzani msewu anthu inu! Lambulani msewu.+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”+
14 Ndiyeno wina adzati, ‘Anthu inu, konzani msewu! Konzani msewu anthu inu! Lambulani msewu.+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”+