Yesaya 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+
10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+