Mateyu 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, pa nthawiyo anthu ambiri adzapunthwa+ ndipo adzaperekana ndi kudana.+ Maliko 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amakhala opanda mizu mwa iwo okha, ndipo amapitirizabe kwakanthawi. Koma chisautso kapena mazunzo akangobuka chifukwa cha mawuwo, iwo amapunthwa.+ Luka 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira ndi chimwemwe, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+ 2 Timoteyo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwe ukudziwa kuti anthu onse m’chigawo cha Asia+ andisiya.+ Ena mwa iwo ndi Fugelo ndi Heremogene.
17 Amakhala opanda mizu mwa iwo okha, ndipo amapitirizabe kwakanthawi. Koma chisautso kapena mazunzo akangobuka chifukwa cha mawuwo, iwo amapunthwa.+
13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira ndi chimwemwe, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+
15 Iwe ukudziwa kuti anthu onse m’chigawo cha Asia+ andisiya.+ Ena mwa iwo ndi Fugelo ndi Heremogene.