1 Akorinto 14:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma zinthu zonse zizichitika moyenera ndi mwadongosolo.+ Agalatiya 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngati tikukhala mwa mzimu, tiyeninso tipitirize kuyenda motsogoleredwa ndi mzimuwo.+ Akolose 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza ngakhale kuti sindili kumeneko, ndili nanu ndithu mumzimu.+ Ndine wosangalala poona kuti mumachita zinthu mwadongosolo,+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro+ cholimba mwa Khristu.
5 Popeza ngakhale kuti sindili kumeneko, ndili nanu ndithu mumzimu.+ Ndine wosangalala poona kuti mumachita zinthu mwadongosolo,+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro+ cholimba mwa Khristu.