1 Akorinto 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pakuti Mulungu si Mulungu wachisokonezo,+ koma wamtendere.+ Mofanana ndi m’mipingo yonse ya oyerawo, Akolose 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza ngakhale kuti sindili kumeneko, ndili nanu ndithu mumzimu.+ Ndine wosangalala poona kuti mumachita zinthu mwadongosolo,+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro+ cholimba mwa Khristu.
33 Pakuti Mulungu si Mulungu wachisokonezo,+ koma wamtendere.+ Mofanana ndi m’mipingo yonse ya oyerawo,
5 Popeza ngakhale kuti sindili kumeneko, ndili nanu ndithu mumzimu.+ Ndine wosangalala poona kuti mumachita zinthu mwadongosolo,+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro+ cholimba mwa Khristu.