Machitidwe 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano. 1 Akorinto 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ineyo pandekha, ngakhale kuti mwa thupi sindili kumeneko koma mu mzimu ndili komweko, ndamuweruza kale+ ndithu munthu amene wachita zimenezi, ngati kuti ndinali nanu kumeneko.
16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano.
3 Ineyo pandekha, ngakhale kuti mwa thupi sindili kumeneko koma mu mzimu ndili komweko, ndamuweruza kale+ ndithu munthu amene wachita zimenezi, ngati kuti ndinali nanu kumeneko.