Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+ Yesaya 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti Yehova wanena kuti: “Ndidzamupatsa mtendere ngati mtsinje+ ndi ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira,+ ndipo inu mudzayamwadi.+ Adzakunyamulani m’manja ndipo adzakusisitani mwachikondi atakuikani pamwendo.+ Aroma 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu amene amapereka chiyembekezo akudzazeni ndi chimwemwe chonse ndi mtendere wonse chifukwa cha kukhulupirira kwanu, kuti mukhale ndi chiyembekezo chachikulu mwa mphamvu ya mzimu woyera.+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
12 Pakuti Yehova wanena kuti: “Ndidzamupatsa mtendere ngati mtsinje+ ndi ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira,+ ndipo inu mudzayamwadi.+ Adzakunyamulani m’manja ndipo adzakusisitani mwachikondi atakuikani pamwendo.+
13 Mulungu amene amapereka chiyembekezo akudzazeni ndi chimwemwe chonse ndi mtendere wonse chifukwa cha kukhulupirira kwanu, kuti mukhale ndi chiyembekezo chachikulu mwa mphamvu ya mzimu woyera.+