Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge. Machitidwe 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthuyu ataona Petulo ndi Yohane ali pafupi kulowa m’kachisimo anayamba kupempha kuti amupatse mphatso zachifundo.+
33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.
3 Munthuyu ataona Petulo ndi Yohane ali pafupi kulowa m’kachisimo anayamba kupempha kuti amupatse mphatso zachifundo.+