Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Yesaya 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, ife tayembekezera inu pofunafuna njira yanu ya chilungamo.+ Mtima wathu wakhala ukulakalaka kuti ukumbukire dzina lanu, ndi zimene dzinalo limaimira.+
7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+
8 Inu Yehova, ife tayembekezera inu pofunafuna njira yanu ya chilungamo.+ Mtima wathu wakhala ukulakalaka kuti ukumbukire dzina lanu, ndi zimene dzinalo limaimira.+