Salimo 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+ Salimo 69:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Afafanizidwe m’buku la anthu amoyo,+Ndipo iwo asalembedwe m’bukumo pamodzi ndi anthu olungama.+ Salimo 139:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa.
8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+
16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa.