Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+ Yobu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione. Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+
21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+
18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione. Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+