1 Mbiri 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ndi ana awo anali kuyang’anira zipata za nyumba ya Yehova, kapena kuti chihema chopatulika,* ndipo ankachita utumiki waulonda.+ 1 Mbiri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamng’ono ndi wamkulu potsata nyumba za makolo awo,+ kuti apeze ogwira ntchito pachipata chilichonse.
23 Iwo ndi ana awo anali kuyang’anira zipata za nyumba ya Yehova, kapena kuti chihema chopatulika,* ndipo ankachita utumiki waulonda.+
13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamng’ono ndi wamkulu potsata nyumba za makolo awo,+ kuti apeze ogwira ntchito pachipata chilichonse.