32 Ana a Leviwa analinso ndi ntchito yolondera+ chihema chokumanako, malo oyera,+ ndiponso yolondera abale awo, ana a Aroni, pa utumiki wa panyumba ya Yehova.+
45 Choncho ansembe ndi Alevi pamodzi ndi oimba+ ndi alonda a pazipata+ anayamba kusamalira udindo+ wawo kwa Mulungu ndi kusunga lamulo lakuti azikhala oyera,+ malinga ndi lamulo la Davide ndi mwana wake Solomo.