1 Mbiri 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usiku anali kukhala mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa anali pa utumiki wawo waulonda.+ Iwo ndiwo anali kusunga kiyi kuti azitsegula zipata m’mawa uliwonse.+
27 Usiku anali kukhala mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa anali pa utumiki wawo waulonda.+ Iwo ndiwo anali kusunga kiyi kuti azitsegula zipata m’mawa uliwonse.+