Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Samueli anagonabe mpaka m’mawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova,+ koma anaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.+

  • Malaki 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Ndani pakati panu amene angatseke zitseko za kachisi popanda malipiro?+ Anthu inu mumayatsa moto paguwa langa lansembe kuti mulandire malipiro.+ Ine sindikukondwera nanu, ndipo nsembe zanu zimene mukupereka monga mphatso sizikundisangalatsa,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena