2 Mbiri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno muchite izi: Gawo limodzi mwa magawo atatu a ansembe+ ndi Alevi+ amene ali pakati panu omwe adzabwere pa sabata,+ lidzakhale alonda a pamakomo.+
4 Ndiyeno muchite izi: Gawo limodzi mwa magawo atatu a ansembe+ ndi Alevi+ amene ali pakati panu omwe adzabwere pa sabata,+ lidzakhale alonda a pamakomo.+