2 Mbiri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho muchite izi: Mukhale mʼmagulu atatu ofanana a ansembe ndi Alevi, amene adzabwere kudzagwira ntchito+ pa Sabata, ndipo gulu limodzi lidzakhale alonda apamakomo.+
4 Choncho muchite izi: Mukhale mʼmagulu atatu ofanana a ansembe ndi Alevi, amene adzabwere kudzagwira ntchito+ pa Sabata, ndipo gulu limodzi lidzakhale alonda apamakomo.+