1 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli. 1 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zili choncho, mwanayo Samueli anali kutumikira+ Yehova pamaso pa Eli, ndipo mawu a Yehova+ anali osowa masiku amenewo,+ moti masomphenya sanali kuonekaoneka.+
11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli.
3 Zili choncho, mwanayo Samueli anali kutumikira+ Yehova pamaso pa Eli, ndipo mawu a Yehova+ anali osowa masiku amenewo,+ moti masomphenya sanali kuonekaoneka.+