Levitiko 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndipo moto unatsika kuchokera kwa Yehova+ n’kunyeketsa nsembe yopsereza ndiponso mafuta, zimene zinali paguwa lansembe. Anthu onse ataona zimenezi, anayamba kufuula mokondwera+ ndipo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi. 1 Mbiri 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Davide anamangira Yehova guwa lansembe pamalopo,+ ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Komanso anaitana pa dzina la Yehova+ yemwe tsopano anamuyankha ndi moto+ wochokera kumwamba umene unafika paguwa lansembe yopsereza. 2 Mbiri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera,+ moto unatsika kuchokera kumwamba.+ Motowo unanyeketsa nsembe yopsereza+ pamodzi ndi nsembe zina, ndipo ulemerero wa Yehova+ unadzaza nyumbayo.
24 ndipo moto unatsika kuchokera kwa Yehova+ n’kunyeketsa nsembe yopsereza ndiponso mafuta, zimene zinali paguwa lansembe. Anthu onse ataona zimenezi, anayamba kufuula mokondwera+ ndipo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.
26 Ndiyeno Davide anamangira Yehova guwa lansembe pamalopo,+ ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Komanso anaitana pa dzina la Yehova+ yemwe tsopano anamuyankha ndi moto+ wochokera kumwamba umene unafika paguwa lansembe yopsereza.
7 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera,+ moto unatsika kuchokera kumwamba.+ Motowo unanyeketsa nsembe yopsereza+ pamodzi ndi nsembe zina, ndipo ulemerero wa Yehova+ unadzaza nyumbayo.