Ekisodo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+ 2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.
25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.