-
Yoswa 8:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Anamanga guwalo mogwirizana ndi zimene Mose mtumiki wa Yehova analamula ana a Isiraeli, monga mwa zolembedwa m’buku la chilamulo+ cha Mose, zimene zimati: “Guwa lansembe la miyala yathunthu, yosasema ndi chipangizo chachitsulo.”+ Ndipo iwo anaperekerapo kwa Yehova nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano.+
-