Ekisodo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+ Deuteronomo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzipereka nsembe zachiyanjano+ ndi kuzidyera pamenepo,+ ndipo muzikondwera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+
24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+
7 Muzipereka nsembe zachiyanjano+ ndi kuzidyera pamenepo,+ ndipo muzikondwera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+